“Koma iwe uziphunzitsa zogwirizana ndi chiphunzitso choona.”

Tito 2:1

Zaposachedwa

"Ine sindichita manyazi ndi Uthenga Wabwino chifukwa ndiwo mphamvu za Mulungu zopulumutsa aliyense amene akhulupirira."

Aroma 1:16

“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”

Salimo 86:11

Ulaliki Waposachedwa

Mlaliki

Dr. Joshua Hutchens

Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi Mtsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr Hutchens watumikirapo mipingo iwiri mu mzinda wa United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.

“Koma kulani mu chisomo ndi mʼchidziwitso cha Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.”

2 Petro 3:18

Ulaliki Waposachedwa

Mlaliki

Isaac Dzimbiri

Mbusa Dzimbiri amatsogolera kapembezedwe ku Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso amatumikira alimodzi ndi Euro-African Baptist Mission yomwe yiri ku Zomba Malawi. M’busa Dzimbiri watumikira mipingo ya ku Malawi komanso ya ku Zambia, ndipo ali ndi M.A. mu maphunziro a zautumiki kuchokera ku Central Africa Baptist University ndi Piedmont International University.

Zithandizo Zambiri