
1 | Mulungu ndi wabwino
Mulungu ndi Mlengi wathu wabwino ndi Mfumu. Mulungu adakulenga iwe kuti ukhale naye komanso ndi kumamukonda iye.
Mulungu ndi Mlengi wathu wabwino ndi Mfumu. Mulungu adakulenga iwe kuti ukhale naye komanso ndi kumamukonda iye.
Iwe udachimwila Mulungu, amene ali Mlengi wabwino ndi Mfumu. Chifukwa chakiti Mulungu ndi wabwino, adzalanga tchimo lanu ndi imfa yamuyaya kuchionongeko.
Yesu sadachimwe ingakhalale tchimo lalingóno. Yesu adafela machimo athu. Mulungu adaukitsa Yesu kwa akufa.
Ngati uvomereza ndi kukhulupirira, Mulungu adzakupatsa iwe mphanzo ziwiri: kulungamitsidwa ndi chipulumutso.
Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.