6 | Perekani ku Mpingo Wanu

Gawani


Timapereka chifukwa Mulungu anatipatsa ife Mwana wake. Tikuyenera kukhala ndi dogosolo la kupereka kwathu komanso tikuyenera kupeka wokondwera.

We give because God gave us his Son. We need to plan our giving and to give cheerfully.