
Kumvera Mulungu ndi Malamulo ake/Obedient to God and his commandment
1 Yohane 2:3-11, Buku la 1 Yohane likupitiriza kubwera poyera njira zomwe khristu opulumutsidwa akuyenera kupitiriza kuyenda pa nthawi imene khristu wapulumutsidwa. Kumvera mulungu ndi