Kuyenda m'Choonadi

Dr. Joshua Hutchens

Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu. ​

Ulaliki

“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”

Salimo 86:11

M'ndandanda Opitilira