2 | Iwe ndiwe wochimwa

Gawani

Iwe udachimwila Mulungu, amene ali Mlengi wabwino ndi Mfumu.

Aroma 3:23, “Pakuti onse anachimwa naperewera pa ulemerero wa Mulungu.”

Kodi umaganiza kuti ndi we munthu wabwino? Udalepherapo kumvera malamulo khumi ndi limodzi (Eksodo 20)?

  • Lemekeza atate wako ndi amayi ako.
  • Usaphe
  • Usachite chigololo
  • Usabe
  • Usaperekere umboni onama
  • Usasilira

 

Chifukwa chakiti Mulungu ndi wabwino, adzalanga tchimo lanu ndi imfa yamuyaya kuchionongeko.

Aroma 6:23, “Pakuti malipiro a tchimo ndi imfa, koma mphatso yaulere imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha mwa Khristu Yesu Ambuye athu.”