4 | Vomereza ndi Kukhulupirira

Gawani

Aroma 10:9–10, “Kuti ngati udzavomereza ndi pakamwa pako kuti, ‘Yesu ndiye Ambuye,’ ndi kukhulupirira mu mtima mwako kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa, udzapulumuka. Pakuti ndi mtima wanu mukhulupirira ndi kulungamitsidwa, ndipo ndi pakamwa panu muvomereza ndi kupulumutsidwa.”

 Ngati uvomereza ndi kukhulupirira, Mulungu adzakupatsa iwe mphanzo ziwiri.

  1. Kulungamitsidwa. Mulungu adzakukhululukira ndi kukusitha.
  2. Chipulumutso. Mulungu adzakupulumutsa kuchionongeko ndi kukupatsa moyo wosatha uli naye.

Kuvomereza kuti “Yesu ndi Ambuye” ndi kutembenuka mbuyo tchimo.

Kukhulupirira ndi kudalira zomwe Yesu adachita chifukwa cha iwe.