Mayitanidwe a Abrahamu/The calling of Abraham

Gawani

Genesis 12:1-3, Mulungu akumuyitana Abrahamu amene akuchokera ku dziko lomwe amapembeza mafano. Mulungu akuyitana Abrahamu yemwe anali opanda kanthu kalikonse pamaso pa mulungu, ndi kuchita naye malonjezo akunthawi zosatha. Abrahamu anakhulupirira mulungu ndi malonjezo ake. Lero ife ngati akhristu kodi takonzeka kusiya ntchito za mum’dima ndi kutsatira mayitanidwe athu omwe mulungu watiyitana nawo. Mulungu walonjeza moyo wosatha mwa Yesu Khristu, Kodi ife tili okonzeka kulandira moyowu?

Genesis 12:1-3, God is calling Abraham who was coming from a place of idol worshiping. God calls Abraham who could offer God nothing and God made everlasting promises to him and to his offspring. Abraham put faith in God and his promises and it was counted righteous to him. Today christians have the same opportunities of adhering to God’s calling, but still, are ready to leave everything behind and follow him?