Pemphero ndi kuthamangira/Prayer and pursuit

Gawani

1 Yohane 5:16,17 mu mpingo, pamene membala wachita tchimo ndi udindo wa abale ndi alongo mu mpingo kuthandiza m’baleyu kuti alape tchimo wachitaro ndi kubwerera kwa mulungu. Komanso pamene tchimo lachitidwa pamaso pa mpingo onse ndi udindo wa mpingo ku pempherera m’bale ameneyu ndi kumuthamangira kuti abwezedwe ndi kuyamba kuyenda m’choonadi. Izi ziyenera kuchitidwa mwa chikondi pofuna kuonetsera chikondi kwa abale ndi alongo mu mpingo.

1 John 5:16-17 in the church, when a member has committed a sin it is the responsibility of the fellow brothers and sisters to help this member to repent and turn to God again. As a church, the body of Christ we kindly correct a brother or sister who has committed such sin in the church and help them to repent and turn to God again. We do this so lovingly to show that we care about them and we want them to repent and turn to God to continue receiving God’s love.