
Uthenga Wabwino ndi Mphamvu ya Mulungu
Aroma 1:16–17. Uthenga Wabwino ndi mphamvu ya Mulungu yopulumutsa chifukwa mu Uthenga Wabwino mphatso ya Mulungu ya chilungamo ya onetsedwa.
Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.
Aroma 1:16–17. Uthenga Wabwino ndi mphamvu ya Mulungu yopulumutsa chifukwa mu Uthenga Wabwino mphatso ya Mulungu ya chilungamo ya onetsedwa.
Aroma 1:8–15. Chigonjetso cha Mwana wa Mulungu chitha kuonekera mu chikhulupiriro chathu komanso mukulalikira Uthenga Wabwino ku mayiko onse.
Aroma 1:1–7. Mulungu adatipatulidwa ife kuti tikalalikire Uthenga Wabwino ku mitundu yonse kwa ulemerero wa dzina la Mulungu.
“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”
Salimo 86:11