Chikondi pa wina ndi mnzake ndi m’choonadi/Love for one another and in truth
Love for one another and in truth
Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.
Love for one another and in truth
Khalani mwa Khristu/Remain in christ
1 Yohane 2:3-11, Buku la 1 Yohane likupitiriza kubwera poyera njira zomwe khristu opulumutsidwa akuyenera kupitiriza kuyenda pa nthawi imene khristu wapulumutsidwa. Kumvera mulungu ndi
1 Yohane 1:5-2:2, kutchulidwa kuti nkhristu sikungapangise munthu kukhala ndi zimene nkhristu ali nazo. Bukuli muli njira zomwe akhristu akuyenera kuyenda pa chikhristu chawo. Chiyambi
1 Yohane 1:1-4, moyo weniweni umachokera kwa mulungu ndipo ndi moyo wosatha. Kodi ife tili ndi moyo wosatha? Mulungu amapereka moyo wosatha, ndiye Yesu Khristu.
Za mkati mwa buku la 1 Yohane/Inside the book of 1 John
Mtima ngati wa Khristu Yesu/A heart like that of Christ Jesus
Kuyenda m’chikondi/Walking in the love
“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”
Salimo 86:11