Wilkes Watch
M’busa Watch ndi yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist ndipo amagwira ntchito ndi Euro-Africa Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Asanayambitse mpingo wa Gospel Life Baptist limodzi ndi Dr. Hutchens, M’busa Watch anali m’busa wa Mpingo wa Baptist ku Phiri la Ntonya kwa dzaka zisanu. Iye ndi mkazi wake Eunice ali ndi ana awiri akazi.
Yesu Khristu mwini Chilamulo komanso mpulumutsi wa anthu onse/Jesus Christ the fulfilment of the law and savior of all people
Kumwalira kwa Sara/The death of Sarah
Abrahamu kapolo wodzipereka/Abraham a devoted servant
Tchimo silisintha kukhala choonadi/ A lie cannot change to be the truth
Mulungu ndi wabwino ndi wolungama/God is good and righteous
Kukhulupirika kwa Malonjezo a Mulungu/The Faithfulness of God's Promises
Mdalitso Wochokera Kwa Mulungu yehovah Kupita kwa ana oyamba a Adamu ndi zotsatira zake/Jehovah's blessings upon Adam's children and their response.