Yesu auka mmanda/Jesus is raised from the tomb

Gawani

Yohane 20:1-18, Yesu anakwanilitsa zonse zomwe anabwerera kuzachita padziko lapansi. Yesu anakwanitsa kulipira ngongole ya machimo yomwe ife sitikanakwanitsa kulipira patokha. Yesu ali m’manda mulungu anamukitsa kwa akufa pakuti iye anali olungama ndipo sanayenera kuti thupi lake lichite chivundi. Tsopano lino ali kumwamba kwa atate ake ndi atate athu, mulungu wake komanso mulungu wathu. Ndikudzera mwa iye tsopano tithakutsendera chifupi ndi mpando wa chisomo cha mulungu.

John 20:1-18, Jesus fulfilled all that he came to do on earth. Jesus payed the ransom for our sins something that we could not do on our own. Jesus when in the tomb, God could not let his body to decay for he was righteous. So he resurrected him. Now he is in heaven with his father and our father, his God and our God. And now we can with confidence approach the throne of grace of our God.