8 | Kondani Anthu Ena Dr. Joshua Hutchens August 5, 2020 Dziko lidzadziwa kuti ndife ana aMulungu kudzera mu chikondi chathu. Baibulo likutilamulira ife kuti tikonde Mulungu, anasi utuu, wina ndi m’dzake, adani athu, komanso iwu omwe ndi osowa. Phunzirani »
Mphamvu za Mulungu Zosunga Oyera Mtima Isaac Dzimbiri May 11, 2020 Chifukwa cha mphamvu za Mulungu ndi chifuniro chake, anthu woyera mtima apirira mu chikulupirira chawo mpaka kumapeto kwa moyo. Phunzirani »