6 | Perekani ku Mpingo Wanu Dr. Joshua Hutchens August 5, 2020 Timapereka chifukwa Mulungu anatipatsa ife Mwana wake. Tikuyenera kukhala ndi dogosolo la kupereka kwathu komanso tikuyenera kupeka wokondwera. Phunzirani »
1 | Timagwira ntchito chifukwa Mulungu akugwira ntchito Dr. Joshua Hutchens April 28, 2020 Mulungu wakulenga iwe kukhala watsopano. Tsono timamvera Mulungu chifukwa timamukonda Mulunguyo, ndipo timamumvera, Mulungu amagwira ntchito mwaife. Phunzirani »