Machitidwe a Atumwi

1 | Minda Inayi

Cholinga chathu ndikupanga ophunzira ndipo timapanga ophunzira polalikira uthenga wabwino ndi kudzala mipingo. Kuti tidzale mpingo timayenera kukonza munda, kudzala mmunda, kusamalira munda kenaka kukolola mmunda.

Phunzirani »

7 | Kuchita Umboni wa Yesu

Mulungu akuyitana mKhristu wina aliyense kukhala mboni ya Yesu. Kuchitira umboni wokhudzana ndi Yesu ndi kosavunga monga kuyakhula nkhani yako ndi nkhani ya Mulungu.

Phunzirani »

5 | Sonkhani Pamodzi kuti Mupembeze

Timasokhana pamodzi kuti tipembeze ndi cholinga choti tithandizone wina ndi nzake kukula musinkhu mwa Khristu. Tikuyenera kukhala ndi chikhalidwe chopembera ndi mpingo umodzi nthawi zonse.

Phunzirani »

4 | Werenga Baibulo

Kudzera mukuwerenga Baibulo, timamva Mulungu akuyakhula nafe. Khalani ndi dogosolo lakawerenge ka Baibulo komanso yambani kuwerenga.

Phunzirani »

3 | Yambani Kupemphera

Kudzera mupemphero, timamva umwana wathu mubanja la Mulungu. Yesu anatiphuzitsa momwe tikuyenerera kupemphera munjira yomwe ikuyenerera ku pereka ulemerero kwa Mulungu.

Phunzirani »

2 | Batizidwani

Ubatizo ndi njira yoyambirira ya kumvera monga mKhristu watsopano. Uma onetsera kwa aliyense yemwe alikunja zomwe Mulungu wachita kuti mwa munthu.

Phunzirani »