4 | Werenga Baibulo Dr. Joshua Hutchens May 15, 2020 Kudzera mukuwerenga Baibulo, timamva Mulungu akuyakhula nafe. Khalani ndi dogosolo lakawerenge ka Baibulo komanso yambani kuwerenga. Phunzirani »
Chikondi cha Mulungu Chitsimikiza Kupirira kwa Oyera Mtima m’Chikhulupiriro Isaac Dzimbiri May 2, 2020 2 Timoteyo 1:9. Kupirira kwa anthu wokhulupirira kwa khazikika mu chikondi chosatha cha Mulungu, yemwe anatipatiratu chisomo chake mwa Yesu Khristu kutiwombola ife ku machimo athu. Phunzirani »