Petro anavomereza za Yesu/Peter’s confession of Jesus

Gawani

Mateyu 16:5-18 Yesu atafunsa ophunzira ake kuti iwo amati Yesu ndi ndani, Petro anayankha kuti “inu ndi Khristu mwana wa Mulungu wa moyo.”Ndipo ulendo wa Petro oyenda ndi Khristu unayambika. Kodi ife ngati akhristu timati Yesu ndi ndani? Nkhristu yemwe ndi opulumutsidwa akuyenera kukwanitsa kuyankha funso limeneli ponena kuti “Yesu ndi Khristu mwana wa mulungu ndi ambuye ndi mpulumutsi wa moyo wa aliyense.”

Matthew 16:5-18 Jesus posed a question to his disciples, he asked “who do you say that I am?” Peter answered without any hesitation that ‘you are Christ the son of the living God.’ As christians today we should be able to answer that question when its posed to us as well. We confidently say that Jesus is the Messiah, truly God and truly man and he the lord and saviour of our lives.