Anapereka mzimu wake/He gave up his spirit

Gawani

Yohane 19:30, pamene Yesu anali pamtanda kusausitsa kuti apume, anayangána kumwamba kwa atate ake nati “kwatha.” Chinthu china chodabwitsa chinachitika patatha izi. Pamene ife anthu tikamwalira mizimu yathu imatengedwa kwa ife. Koma Yesu anapereka mzimu wake yekha. Imfa yake imapangitsa kuthekera kati ife tikhale opanda mantha ingakhale mavuto abwera.

John 19:30, when Jesus was at the cross gasping for air, he looked up to his father and called out it is “finished.” One remarkable thing happened afterthat. When we die our spirit is taken away from us but Jesus gave up his spirit. The death of Jesus makes it possible for us that we no longer live in fear even in the face of problems.