Ana A Mulungu/The Children Of God

Gawani

1 Yohane 2:28-3:1-10, mawu a mulungu awa akuthandiza onse omwe ndi ake mulungu kuzindikira kuti pamene ife tagulidwa ndi mwazi wake wa Yesu khristu ndife tsopano ana a mulungu. Ana a mulungu amachita chilungamo ndipo ndiwolungama. Onse omwe alimwa khristu amafanana naye iye. Koma ngati pakati pathu pali ena omwe sachita chilungamo ngakhalenso sakonda m’bale wawo, amenewo siake a mulungu koma a mdierekezi.

1 John 2:28-3:1-10, these words of God are helping us all, children of God to realise that when we were bought by the blood of Christ Jesus, we became his. And now we are known as children of God. The children of God are evident by this fact that whoever does practice righteousness and is just belongs to God. But if one does not, even to love his brother becomes a problem for him then he is of the Devil.