Kumvera Mulungu ndi Malamulo ake/Obedient to God and his commandment

Gawani

1 Yohane 2:3-11, Buku la 1 Yohane likupitiriza kubwera poyera njira zomwe khristu opulumutsidwa akuyenera kupitiriza kuyenda pa nthawi imene khristu wapulumutsidwa. Kumvera mulungu ndi malamulo ake ndi chiwonetsero chachikulu ndi chilungamo chathu kwa anthu kuti ife timankonda mulungu, timakhulupirira mulungu wathu, zonse zimene mulungu atilamulira kuti tichite ife timamvera ndikuchita.

1 John 2:3-11, the book of 1 John continues to shade light on principles that true christians are continuously to show in the congregation and to the people who are not part of the church and are regarded as non believers. Obedient to God and his principles shows a sign and our justice to others that we love God and that we obey his principles and all that God commands us we willingly do.