Mpingo ndi thupi la Khristu Yesu/A church is the body of Christ Jesus

Gawani


Afilipi 2:1-4, mundime yamalemba imeneyi Paulo akuthokoza, akulangiza, akulimbikitsa ndi kudzuzura mpingo omwe iye anawuyambitsa ponena kuti “monga mpingo ndi thupi la Khristu Yesu, ziwalo zake kukhala akhristu sakuyenera kukhala ndi migawano, popeza sitingathe kugawa thupi la Khristu Yesu.” Motero akulimbikitsa akhristu kukhala ozichepetsa mu mpingo.

Philippians 2:1-4, in this passage Paul is extending his gratitude, encouragement, advice and his rebuke to the church he started by saying “as the church is the body of Christ Jesus, its members being the Christians are not suppose to have divisions in the church, just as we cannot divide the body of Christ Jesus.” So he is encouraging christians to have humility in the church.