Kodi muli mbali iti m’masiku omalizawa?/What side are you on in these ladder days?

Gawani

Chivumbulutso chaputara 7, mu chaputara chimenechi Dr. Eric akupitiliza kubweletsa poyera za nsautso waukulu m’masiku omaliza. Kamvetsetsedwe ka nthawiyi kakupitilirabe kukhala kovutirapo kwa anthu ena kamba kuti kalembedwe kozembayisa kakupitilirabe kupezeka ingakhale mu chaputarachi. Panthawi yomweyo tikuona kuti Paulo akulemba chaputarachi mundondomeko yomwe ingafananizilidwe ndi mapiri omwe patali akuoneka ngati Phiri limodzi koma pomwe uwandikira ndipomwe ungazindikire kuti ndi mapiri omwe akupezeka mondondozana. Zinthu zochitika m’masiku omalizawa zikupezeka zomwe zikutchulidwa kuti zimatiro zisanu ndi ziwiri zomwenso kalembedwe kake ndi kozembayisa. Munthawi imeneyi ndichanzeru kuzifunsa kuti kodi tili mbali iti? popeza nthawi nde yatha kale.

Revelation chapter 7, in this chapter Dr. Eric continues to explore the great tribulation in the ladder days. The understanding of the ladder days and the great tribulation continues to be hard to others as the chapter continues to have the writings that uses the metaphoric language. And at the very time, we see that Paul is writing the chapter in a loop which also can be liken to mountains, from afar, they look like one big mountain but as you get closer and closer, you begin to see that they are but many mountains as you move along them. The great tribulation is also told in the way that the seven scrolls unfolds. At this point it is right to ask the question what side are you on? as we see the days drawing near to the end.