Za mkati mwa buku la 1 Yohane/Inside the book of 1 John

Gawani

1 Yohane, buku limeneli likupezeka ndi uthenga opasa moyo. Nkhani zomwe zikupezeka mu bukuli kwambiri ndi ndondomeko za kayendedwe ka khristu kuti ndi ziti zomwe akuyenera kuchita khristu komanso ndi ziti zomwe sakuyenera kuchita pamene iye wa pulumutsidwa kapena pamene iye watchulidwa kuti ndi khristu. Khristu aliyense amakhala khristu pamene wabatizidwa ndipo pamene mzimu woyera ali mwa iye. Ndondomeko yomwe ili mu bukuli ikuthandizira akhristu kuzindikira kuti tsopano ndife akhristu pamene mzimu woyera ali mwa ife.

1 John, this book contains the word of life. This book is mainly about the way of life of christians. It comprises of what christians are suppose to do and are not suppose to do when are saved and have now received the Holy Spirit and are announced as christians. Every person becomes a christian when have been baptised and have received the Holy Spirit because nobody is born that way. So this book it’s all about how can a christian recognise the power of the Holy Spirit operating in him or her and one is able to bare good fruits.