Chikondi pa wina ndi mnzake ndi m’choonadi/Love for one another and in truth

Gawani

1 Yohane 3:11-18, mawu awa akutikumbutsa za chikondi chathu pa wina ndi mnzake makamaka pamene ife tsono ndi ake a mulungu, chikondi chathu chisakhale cha pakamwa koma cha ntchito zathu ndi m’choonadi kuwonetsera chiyanjano chathu ndi mulungu wathu mwa ambuye wathu Yesu Khristu.

1 John 3:11-18, these words are reminding us of our love for one another especially now that we are children of God, our love for each other should not be in words only but in works also and in truth showing our fellowship with God through our lord Jesus Christ.