6 | Chulukitsani Alimi

Gawani


Pamene tapanga ophunzira, tiziyembekezera ophunzira atsopano kupanganganso ophunzira ochuluka. Pamene tawazindikira, tikuyenera kuwaphunzitsa komanso kuwatumiza ophunzira atsopanowa. Tikatero timakhala kuti tatumiza alimi ochulukira m’minda ku ntchito yodzala mipingo.

When we make disciples, we should expect new disciples to make more disciples. When we identify, invest in, and send out these new disciples, we send more farmers into other fields for the work of church planting.