Kuyenda mu kuwunika(khalidwe loyamba)/Walking in the light(the first attribute)

Gawani

1 Yohane 1:5-2:2, kutchulidwa kuti nkhristu sikungapangise munthu kukhala ndi zimene nkhristu ali nazo. Bukuli muli njira zomwe akhristu akuyenera kuyenda pa chikhristu chawo. Chiyambi cha bukuli tikupeza chiphunzitso cha moyo. Akhristu amene alandira moyo ndipo ali ndi moyo tsopano akuyenera kuyenda mu kuwunika chifukwa ali pa chiyanjano ndi mulungu amene ndi kuwunika.

1 John 1:5-2:2, to be called a christian cannot make one get all the things a christian has. In this book, many ways are listed for christians to follow when walking in their christianity. The beginning of this book, we read about life. Christians who have received life and now they have life are suppose to walk in the light because they have fellowship with God who is light.