Iwe udachimwila Mulungu, amene ali Mlengi wabwino ndi Mfumu.
Aroma 3:23, “Pakuti onse anachimwa naperewera pa ulemerero wa Mulungu.”
Kodi umaganiza kuti ndi we munthu wabwino? Udalepherapo kumvera malamulo khumi ndi limodzi (Eksodo 20)?
- Lemekeza atate wako ndi amayi ako.
- Usaphe
- Usachite chigololo
- Usabe
- Usaperekere umboni onama
- Usasilira
Chifukwa chakiti Mulungu ndi wabwino, adzalanga tchimo lanu ndi imfa yamuyaya kuchionongeko.
Aroma 6:23, “Pakuti malipiro a tchimo ndi imfa, koma mphatso yaulere imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha mwa Khristu Yesu Ambuye athu.”