Mdalitso wochokera kwa Mulungu kupita kwa ana a Adamu ndi zotsatira zake/Blessings from God upon Adam’s children and their response

Gawani


Mulungu akudalitsa Kaini ndi Abele panthawi yomwe agwira ntchito zawo ndipo iwo akulandira zotsatira zabwino kuchokera ku ntchito zawozi. Panthawi yomweyo tikuona kuthokoza kosiyana komwe kukubwera kuchokera kwa anthu awiriwa omwe agwira ntchito zosiyana pomwe apeleka nsembe zawo kwa Mulungu.

God blesses Cain and Abel when doing their separate work and are blessed abundantly while on the other hand we see how they thank God by offering up sacrifices but with different attitudes