Mdalitso Wochokera Kwa Mulungu yehovah Kupita kwa ana oyamba a Adamu ndi zotsatira zake/Jehovah’s blessings upon Adam’s children and their response.
Mulungu akudalitsa Kaini komanso Abele panthawi yomwe agwira ntchito zawo ndipo akulandira zotsatira zabwino kuchokera ku ntchto zawozo. Panthawi yomweyo tikuona kuthokoza kosiyana komwe kukubwera