Kutsindikizidwa ndi Mzimu Woyera Isaac Dzimbiri August 5, 2020 Mulungu watitsindikiza ndi Mzimu Woyera kutitsimizira kuti chipulumutso chathu ndi chamuyaya. Komanso kuti madalitso onse achipulumutso athu tizalandi kutsogolo. Phunzirani »