
Dongosola la Mulungu pa Chipulumutso cha Oyera Mtima
Aefeso 1:4–7; Aroma 8:29–30. Chipulumutso ya oyera mtima china yamba ndi Mulungu, ndipo chidzamulizidwa ndi Mulungu. Chifukwa choti Mulungu amatsiriza ndogosolo lomwe wa liyamba adzatsirizanso dogosolo la chipulumutso cha oyera mtima.