8 | Kondani Anthu Ena Dr. Joshua Hutchens August 5, 2020 Dziko lidzadziwa kuti ndife ana aMulungu kudzera mu chikondi chathu. Baibulo likutilamulira ife kuti tikonde Mulungu, anasi utuu, wina ndi m’dzake, adani athu, komanso iwu omwe ndi osowa. Phunzirani »