Podcast

6 | Chulukitsani Alimi

Pamene tapanga ophunzira, tiziyembekezera ophunzira atsopano kupanganganso ophunzira ochuluka. Pamene tawazindikira, tikuyenera kuwaphunzitsa komanso kuwatumiza ophunzira atsopanowa. Tikatero timakhala kuti tatumiza alimi ochulukira m’minda ku ntchito yodzala mipingo.

Phunzirani »

4 | Samalirani m’Munda

Monga munda omwe wayamba kukula, akhirisitu atsopano amafunika chisamaliro chauzimu pafupipafupi. Yesu akutilamula kuti tibatize wokhulupirira atsopano ndi kuwaphunzitsa malamulo ake.

Phunzirani »
Titsateni
Magulu

Uthenga Wabwino
Kukhala Wophunzira
Kuyenda m’Choonadi
Kuzama m’Choonadi
Funsa Mafunso

Fufuzani potengera Chiyankhulo
Fufuzani potengera Buku