Yehova akomera mtima Nowa/Jehovah favours Noah

Gawani


Genesis 6:5-8, Kuyipa kwa munthu pa dziko la pansi kumakulirakulirabe ndikuti nthawi zonse amalingalira ndikukhumbira kuchita zoyipa zokhazokha, Yehova anamva chisoni kuti analenga munthu ndikumuyika pa dziko lapansi, ndipo anawawidwa mtima.

Genesis 6:5-8, Consequently ,Jehovah saw that man’s wickedness was great on the earth and that every inclination of the thoughts of his heart was only bad all the time. Jehovah regretted that he had made men on the earth , and his heart was saddened.