Spiritual Warfare/Nkhondo ya uzimu

Gawani

Revelation chapter 8, Dr Eric continues exploring the book of revelation. The book of revelation, for proper understanding of the book, two things to consider; 1) the use of metaphoric language. this is important to take note of, because it would be very difficult to take everything you hear in the book to be literal. for example, when the book talks about the beast of ten horns and the face of a lion, that is metaphoric it’s not literal. 2) the book of revelation is written in a loop, meaning to say its sayings and meanings are constructed in a way that is considered to be known as a loop not linear structuring, thus if you happen to read the book as you would any other books, having the beginning, body then the end, you would miss out everything. In this chapter, we hear of the seven trumpets. These are the judgements God is pouring out on the earth. The judgements goes along, chapters 9, 10, 11 up to 13. And the of exodus helps us to understand more of these judgements by shading the picture of how they are to take place. In chapter 7 of exodus, God frees his people with his majestic hand by using the ten plagues. The same, God will do to free his people once and for all with his hand by the means of the judgements also known as the seven trumpets.

Chivumbulutso 8, Dr Eric akupitiliza kuwunikira zomwe zikuchitika mu buku la chivumbuliutso. Buku la chivumbulutso, kuti munthu ukhale ndi kumvetsesa koyenerera kwa bukuli, njira ziwiri zikuyenera kusatidwa. 1) kagwiritsidwe ntchito ka mizembayiso. bukuli likamakamba za Chilombo cha nyá’nga khumi limodzi ndi khope ya nkango, ndizembayiso umenewo. Kuzilingalira malinga ndi mmowe zikumvekera ndekuti uthenga onse usokonezeka kamvekedwe kake. 2) buku la chivumbulutso linalembedwa mozungulira, mokuti munthu ngati angawerenge bukuli monga achitira mabuku ena omwe amakhala ndi chiyambi kenaka thunthu kumaliza ndi chimaliziro ndekuti uthenga onse waphonyedwa. Mu chaputara cha 8, tkuwuzidwa za malipenga asanu ndi awiri, omwe akuyimirira chiweruzo cha mulungu pa dziko lapansi. Chiweruzochi chikuyenda mu machaputara awa 9, 10, 11 mpaka 13. Komanso buku la exodo 7, limathandiziranso kumvetsesa kowonjezera makamaka momwe chiweruzo chomwe chili mbuku la chivumbulutso chikuchitikira.