Pangano La Mulungu Ndi Nowa/The Covenant Of God With Noah

Gawani

Genesis 9:8-17, Mulungu atakondweretsedwa ndi Nowa chifukwa cha kumvera kwake, anamudalitsa namuuza kuti “abelekane ndipo adzadze dziko lapansi ndikuligonjetsa.” kenaka Mulungu anachita naye pangano Nowa namuuza kuti sazawononganso dziko lapansi ndi madzi. Izi zinali zosangalasa kwa Nowa ndi banja lake. Komatu izi sizikutanthauza kuti Mulungu sazalanganso dziko lapansi chifukwa cha machimo a anthu. Ayi konse, zowona zake n’zakuti, kuli chilango china chomwe chasungilidwa anthu ochimwa chomwe ndi chowopsa kuposa chanthawi ya Nowa.

Genesis 9:8-17, After God was pleased with Noah because of his obedience, he blessed him and told him to “be fruitful and become many and subdue the earth.” Then God went on and made a covenant with Noah. He said ‘never again will I destroy the earth with flooding waters.’ This was good news for Noah and his family. But does that mean that God will never destroy wicked people? Not at all, in fact the bible says that there is a greater judgement restored for those who are wicked and disobedient to God and it is severe than that of Noah.