Nowa ndi chigumula/Noah and the flood

Gawani


Genesis 6:9-22, chiwawa chinadzadza pa dziko lapansi kotero kuti dziko linakhala lowonongeka pamaso pa Mulungu.Izi zinapangisa Mulungu kutsindikadi kwa Nowa kuti sachitiranso mwina koma kuliwononga dziko lapansi ndi zamoyo zonse. Koma Nowa anali munthu wolungama ndiwopanda tchimo pakati pa anthu a m’bado wake. Ndipo Nowa anayenda ndi Mulungu.

Genesis 6:9-22, But the earth had become ruined in the sight of the true God, and the earth was filled with violence. God told Noah that he had decided to put an end to all flesh, because the earth is full of violence on account of them, so I am bringing them to ruin together with the earth. But Noah was a righteous man. He proved himself faultless among his contemporaries. Noah walked with the true God.