Mzimu wachoonadi ndi Mzimu wachinyengo/Spirit of truth and Spirit of Error

Gawani

1 Yohane 4:1-6, Yohane akulembera akhristu kuwachenjeza ku mizimu ya aneneri onama omwe afalikira m’dziko lapansi. Mizimu yachinyengoyi imakana Khristu obwera m’thupi ndi opachikidwa uja. Ngakhale zili choncho akhristu angathe kuzindikira mzimu wochokera kwa mulungu, mzimu umene uvomereza kuti Yesu Khristu anabwera m’thupi ndiwo umene ndiwochokera kwa mulungu.

1 John 4:1-6, John is writing to christians warning them of the false prophets who have gone into the world. These spirits of error reject Christ. Even though it is so, christians can recognise the spirit of truth, the spirit that confess Christ has come in the flesh is from God