Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu/God is greater than our hearts

Gawani

1 Yohane 3:19-24, kulimbika mtima pamaso pa mulungu kumathandiza ife kuzindikira kuti tili pa choonadi ndipo timakhala okhazikika mtima pa maso pa mulungu. Ife timalandira chilichonse tipempha kwa iye, chifukwa timamvera malamulo ake ndi kuchita zimene zimamukondweretsa. Nthawi imene tichita izi; iye amakhala mwa ife ndipo ife timakhala mwa iye.

1 John 3:19-24, as we are strong hearted and stead fast before God, we are helped to realise that we stand in truth and we are at peace within our hearts before God. we receive all that we ask from God, because we listen to him and his commands and do all that he asks of us. All the time as we do this, he lives in us and we live in him.