Makhalidwe a chiyanjano mu mpingo/attributes of fellowship in the church

Gawani

1 Yohane 1:1-4, moyo weniweni umachokera kwa mulungu ndipo ndi moyo wosatha. Kodi ife tili ndi moyo wosatha? Mulungu amapereka moyo wosatha, ndiye Yesu Khristu. Uthenga wabwino umabweretsa chiyanjano pakati pa akhristu mu mpingo. Ngati tili ndi moyo wosatha, tidzakhala pa chiyanjano ndi atate ndi mwana ndi mzimu woyera ndi wina ndi zake. Tikuyenera kukhala ndi chiyanjano chimene ndi moyo wosatha.

1 John 1:1-4, the real life we spoke about, really comes from God and its everlasting life. But do we have everlasting life? God gives his sheep everlasting life and that everlasting life is Jesus Christ. The good news brings about fellowship among christians in the church. If christians have everlasting life, it is evident that they have fellowship with the father, the son, and the Holy Spirit and with their fellow christians.