Kuyipa kwakulu kwa anthu

Gawani


Genesis 6:1-4, ikulongosola za chiyambi chachionongeko cha dziko la pansi ndi chilengedwe chonse chimene Mulungu anachilenga. Mulungu akuononga chilengedwe chonse chomwe anachilenga chifukwa chakuti chilengedwecho (Anthu) chamukana Mulungu.

Genesis 6:1-4, these verses are basically focusing the discussion on the cause of the destruction of the world and its creation. God is rejected by his creation (Humans) thus humans wants to rule themselves instead of being ruled by God.