Kuyenda m’chikondi/Walking in the love

Gawani

Aefeso 4:1-6, Paulo mtumwi akulimbikitsa a khristu kukhala ndi makhalidwe oyenera mayitanidwe awo. Akhale odzichepetsa kwathunthu ndi ofatsa, oleza mtima, ololerana wina ndi mzake. Akhristuwa achite zonsezi moyetsetsa kusunga umodzi wa mzimu umene umatimangilira pamodzi ndi mtendere.

Ephesians 4:1-6, the apostle Paul is appealing to the christians to walk worthily of the calling with which they were called. With all humility and mildness with patience, putting up with one another in love. Earnestly endeavouring to maintain the oneness of the spirit in the uniting bond of peace.