Kondani Mulungu/Love God

Gawani

1 Yohane 2:12-17,chifukwa chachikondi chimene tilinacho pa mulungu wathu, timamumvera ndi kutsatira malamulo ake. Choncho timawonetsera ku dziko lonse kuti ndife ake kudzera muchikondi chomwe tilinacho pa mulungu wathu. Ndichifukwa chake abale tiyeni tipitirize monga okhulupirira komanso okonda mulungu ndi kukana dziko lapansi.

1 John 2:12-17, because of the love we have for God, we continue to love him more. Through our faith, we continue to also obey his commandments. We continue to show the world that we belong to God and that we love him through our living as christians. It is also the reason why brothers, we should continue to love God and continue living as christians and denying the offers of the world.