Kodi umodzi ndi mphamvu?Is oneness a sign of power?

Gawani

Genesis 11:1-9, nthawi zambiri timakamba zokhuza umodzi mokondwera mkumati umodzi ndi mphamvu. Kodi ndi chonchodi? Eya, mokuti Baibulo limalimbikitsa umodzi kufikira pakuti Yesu anati, pali awiri nanenso ndimakhala pomwepo. Koma umodzi omwe ulinga wa Nimurodi, ziwani kuti mulungu amadana nawo ndipo amatsika kuzadzetsa kusamvana pakati pa onse ozondosa zabwino kusandusa zoipa.

Genesis 11:1-9, most of the times we speak of oneness with joy saying, in oneness there is power. But is that true? Yes it is, the Bible encourages oneness to the point that Jesus said, where they’re two people am also there. But the oneness that mimic Nimrod, better know that God hates that and he comes down and cause confusion amongst those who exchanges goodness for badness.