Khalani mwa Khristu/Remain in Christ

Gawani

1 Yohane 2:18-27, nthawi zambiri anthu amafunsa kuti kodi ’tili nthawi ya masiku omaliza?’ Yankho ndi eya. Nthawi ya masiku omaliza ndi pakati pa kubwera kwa Yesu Khristu koyamba ndi kubwera kwa Yesu Khristu kachiwiri. Bukuli likubweretsa poyera nkhani imene ndiyovuta kuyimvetsa. Kodi okana Khristu abwera liti? Paulo akunena motere pakhaniyi, okana Khristu wamkulu adzabwera koma chidwichathu chikhale apa, okana khristu ambiri afika kale. Ndipo ambiri alipakati pathu, mipingo mwadzadza ndi anthu oterewa. Funso nati, kodi ife tili mwa Khristu, kapena gawo lathu ndi lokana Khristu?

1 John 2:18-27, many times people ask in wonder, are we in the ladder days? The answer is yes. The time between the first coming of Jesus Christ an his second coming marks the end of times or the ladder days. This book brings to light about the most confusing story about the anti christ. About the anti christ, When is the anti christ coming? Paul tells us clear that the great anti christ is coming but our focus should be at the anti christ who are already here. many of them are among us, and in our midst they are rejecting christ. But the question still remains, are we remaining in christ or are we partaking the anti christ?