Imfa, Chiwukitso komanso Mapemphero a Yesu Khristu Tsopanolingo

Gawani


Oyera mtima apirira muchikhulupiriro chawo chifukwa imfa ya Yesu yachotsa chostutsa china chilichonse komanso mlandu uliwonse otsutsana ndi sosakhidwa a Mulungu. Chiukitso cha Yesu ndi chitsimikizo cha chikhulupiriro chathu komanso mpemphero ake opemperera oyera mtima amatsimikizira kuti chikhulupiriro cho sichifowoka.