Chipulumutso ya oyera mtima china yamba ndi Mulungu, ndipo chidzamulizidwa ndi Mulungu. Chifukwa choti Mulungu amatsiriza ndogosolo lomwe wa liyamba adzatsirizanso dogosolo la chipulumutso cha oyera mtima.
Mbusa Dzimbiri amatsogolera kapembezedwe ku Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso amatumikira alimodzi ndi Euro-Africa Baptist Mission yomwe yiri ku Zomba Malawi. M’busa Dzimbiri watumikira mipingo ya ku Malawi komanso ya ku Zambia, ndipo ali ndi M.A. mu maphunziro a zautumiki kuchokera ku Central Africa Baptist University ndi Piedmont International University.