Chivumbulutso cha nthawi ya “msautso” m’masiku omaliza/The Revelation of the “great tribulation” in the ladder days

Gawani

Chivumbulutso 6:1-6, Abusa a Eric, akubweletsa poyera za msautso omwe ukuza pa dziko la pansi m’masiku omaliza. M’buku la chivumbulutso chaputara chachisanu ndi chimodzi, chikukamba za zimatiro zisanu ndi ziwiri zomwe kumvetsetsa kwake kumakhala kovutilapo chifukwa cha kagwilitsidwe ntchito ka mawu omwe ndi ozembayisa. Chifukwa chake anthu ambiri amakhala ndi mfundo zosiyanasiyana pa khani imeneyi. Kubweranso kwa Yesu Khristu kachikena kuzakhala ngati momwe koyamba kanalili. Ndipo ma vesi mu chaputarachi akukamba bwino lomwe za zomwe zikuyenera kuchitika m’masiku omaliza Yesu asanabwere.

Revelation 6:1-8, Pastor Eric, brings to light the great tribulation in the ladder days. The book of revelation chapter six, talks about the seven seals where by the language used is metaphoric which is very difficult to understand and this is also the reason why so many people have different views about this very subject. The second coming of Jesus Christ will much be like the first one. And the verses in this chapter explains very well the things to take place before the second coming of Jesus Christ.