Chilungamo ndi Chisomo Adam ndi Hava atachimwa

Gawani


Genesis 3:17-24, mu uthenga uwu tikuona chilungamo cha mulungu chikuonetsedwa chifukwa cha kusamvera kwa Adamu, komanso tikuona mulungu akupeleka chisomo kwa Adamu chifukwa cha chikhulupiriro chake. Chilungamo cha mulungu chinaonekera mu chilango chomwe chinapelekedwa kwa Adamu chifukwa cha tchimo lake. M’dzanja linali tikuona mulungu akuonetsa chisomo kwa Adamu pamene anakhulupirira malonjedzo a mulungu.

Genesis 3:17-24, in this Sermon we see both God’s justice and his grace displayed in response to man’s disobedience and faith respectively. God’s justice is served as judgement is passed on to Adam after his disobedience while on the other hand God responds to Adam’s faith with grace when he shade the blood of an innocent animal to cover their shame which is a shadow of the sacrificial death of Christ.